Artist : Huge kaiya

Artist : Huge kaiyaMkazi ndi maluwa, samachedwa kufota. Mkazi ndi mazila, samachedwa kusweka. Mkazi ndi ofooka, muzelu ndimu thupu. Mawu a mkazi ndilupanga logonjetsa amuna Thupi la mkazi ndi kwinini, lofooketsa amuna Samson wa mphamvu anagonja ndi mkazi David fumu yayikulu, inafoka ndi mkazi Adam first born agonja ndi mkazi A Romeo kupusa anazipha ndi mkazi ifeso ndi ayani kuti tisapusisidwe? Ka huge ndikandani pamaso pa osewa? Cholakwa ndichimodzi mkaziyi sananene.. Chorus Koma nanga bwanji sunanene iwe? Eeeeeeh he eeh!!!!!!!!! Kuti mtima wako sundiziwa ine? Eeeeeeh he eeh!!!!!!!!! Koma nanga bwanji sunadziwe iwe? Eeeeeeh he eeh!!!!!!!!! Kuti mtima wanga umakukonda ine Eeeeeeh he eeh!!!!!!!!! Verse 2 sweetheart, kalilore, mngelo, honey ,dear Ndi dzina liti limene sanatchule? Ndichikondi chiti kwa iye sinafile? Ati ndimuiwale, nde ndiiwale password yanga? Ati mfune wina, nde ndifune nditapeza? ine ndi namwino, azandipeza zikazavuta mkazi ndi kwinini, ofooketsa amuna Samson wa mphamvu anagonja ndi mkazi David fumu yayikulu, inafoka ndi mkazi Adam first born agonja ndi mkazi ka huge ndikandani kuti kasapusisidwe? Cholakwa ndichimodzi mkaziyi sananene.. ( Back to chorus ) Bridge Bwanji sunanene!!!!!!!!! iwe? Kuti mtima wako sundidziwa ine?l